Levitiko 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndidzaika chihema changa chopatulika pakati panu,+ ndipo sindidzanyansidwa nanu.+ Salimo 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu ali pakati pa mzinda.+ Mzindawo sudzagwedezeka.+Mulungu adzauthandiza m’bandakucha.+ Ezekieli 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘“Ndidzachita nawo pangano la mtendere,+ moti adzakhala m’pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.+ Ine ndidzawakhazikitsa m’dzikolo, ndidzawachulukitsa+ ndipo ndidzakhazikitsa malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.+
26 “‘“Ndidzachita nawo pangano la mtendere,+ moti adzakhala m’pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.+ Ine ndidzawakhazikitsa m’dzikolo, ndidzawachulukitsa+ ndipo ndidzakhazikitsa malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.+