Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu kuti akulanditseni+ ndi kupereka adani anu m’manja mwanu.+ Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu ndi kutembenuka n’kuleka kuyenda nanu limodzi.+

  • Salimo 132:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova wasankha Ziyoni,+

      Ndipo amafunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye amati:+

  • Yesaya 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Fuula mwachisangalalo iwe mkazi wokhala mu Ziyoni, pakuti Woyera wa Isiraeli ndi wamkulu pakati pako.”+

  • Hoseya 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Sindidzasonyeza mkwiyo wanga woyaka moto.+ Sindidzawononganso Efuraimu+ pakuti ndine Mulungu+ osati munthu. Ndine Woyera pakati panu+ ndipo sindidzabwera kwa inu nditakwiya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena