Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndipo mundipangire malo opatulika, popeza ndiyenera kukhala pakati panu.+

  • Yoswa 22:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ngati n’zoona kuti dziko lanu n’lodetsedwa,+ wolokerani kudziko la Yehova+ kumene kuli chihema chopatulika cha Yehova,+ mukakhazikike pakati pathu. Koma musapandukire Yehova, ndipo musachititse ifeyo kupanduka chifukwa cha guwa lansembe limene mwamangali, kuwonjezera pa guwa lansembe la Yehova Mulungu wathu.+

  • Ezekieli 37:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “‘“Ndidzachita nawo pangano la mtendere,+ moti adzakhala m’pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.+ Ine ndidzawakhazikitsa m’dzikolo, ndidzawachulukitsa+ ndipo ndidzakhazikitsa malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.+

  • Chivumbulutso 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Taonani! Chihema+ cha Mulungu chili pakati pa anthu. Iye adzakhala pamodzi nawo,+ ndipo iwo adzakhala anthu ake.+ Zoonadi, Mulunguyo adzakhala nawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena