Yeremiya 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kwa iwo kudzamveka mawu oyamikira ndi phokoso la kuseka kwa anthu.+ Ndidzawachulukitsa moti sadzakhala ochepa.+ Ndidzachulukitsa chiwerengero chawo moti sadzakhala kagulu kakang’ono ka anthu.+ Zekariya 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’mabwalo a mzindawo mudzadzaza anyamata ndi atsikana ndipo azidzasewera mmenemo.’”+ Aheberi 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anati: “Kudalitsa, ndidzakudalitsa ndithu, ndipo ndidzakuchulukitsadi.”+
19 Kwa iwo kudzamveka mawu oyamikira ndi phokoso la kuseka kwa anthu.+ Ndidzawachulukitsa moti sadzakhala ochepa.+ Ndidzachulukitsa chiwerengero chawo moti sadzakhala kagulu kakang’ono ka anthu.+