Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 30:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kwa iwo kudzamveka mawu oyamikira ndi phokoso la kuseka kwa anthu.+ Ndidzawachulukitsa moti sadzakhala ochepa.+ Ndidzachulukitsa chiwerengero chawo moti sadzakhala kagulu kakang’ono ka anthu.+

  • Yeremiya 31:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chotero ndidzakumanganso ndipo udzakhazikika,+ iwe namwali wa Isiraeli. Udzanyamula maseche ndi kupita kukavina pamodzi ndi anthu amene akuseka.+

  • Yeremiya 31:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachititsa nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda kukhalanso ndi anthu ochuluka ndiponso ziweto zochuluka,” watero Yehova.+

  • Zekariya 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mngeloyo anauza mnzakeyo kuti: “Thamanga ukauze mnyamata uyo kuti, ‘“Mu Yerusalemu mudzakhala anthu ngati mudzi wopanda mpanda+ chifukwa cha kuchuluka kwa anthu ndi ziweto zimene zili mmenemo.+

  • Mateyu 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Kodi m’badwo uwu ndiufanizire ndi ndani?+ Uli ngati ana aang’ono amene amakhala pansi m’misika n’kumafuulira anzawo osewera nawo+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena