Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo Yehova Mulungu wako adzakuchititsa kukhala ndi zinthu zosefukira pa ntchito iliyonse ya manja ako,+ chipatso cha mimba yako, chipatso cha ziweto zako+ ndi chipatso cha nthaka yako.+ Pamenepo udzatukuka+ chifukwa Yehova adzakondweranso nawe kuti akuchitire zabwino, monga mmene anakondwera ndi makolo ako.+

  • Ezekieli 36:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ine ndidzatembenukira kwa inu ndi kukuthandizani.+ Inu mapiri a ku Isiraeli, ndithu anthu adzalima minda mwa inu ndi kubzala mbewu.+

  • Hoseya 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamenepo ndidzamufesa ngati mbewu zanga padziko lapansi.+ Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo+ ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Inu ndinu anthu anga,”+ ndipo iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+

  • Zekariya 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndidzawamwaza ngati mbewu pakati pa anthu a mitundu ina+ ndipo adzandikumbukira ali kumadera akutali.+ Iwowo ndi ana awo adzapezanso mphamvu ndipo adzabwerera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena