1 Mafumu 8:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 ndiyeno iwo n’kuzindikira kulakwa kwawo m’dziko limene anawatengeralo+ n’kulapa,+ ndipo akapempha+ chifundo kwa inu m’dziko la adani awo amene awagwira,+ n’kunena kuti, ‘Tachimwa,+ tachita zolakwa,+ ndiponso tachita zinthu zoipa,’+ Yeremiya 51:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 “Inu amene mwathawa lupanga, pitirizani kuthawa. Musaime chilili.+ Kumbukirani Yehova+ pamene muli kutali kwambiri ndipo mukumbukirenso Yerusalemu mumtima mwanu.”+
47 ndiyeno iwo n’kuzindikira kulakwa kwawo m’dziko limene anawatengeralo+ n’kulapa,+ ndipo akapempha+ chifundo kwa inu m’dziko la adani awo amene awagwira,+ n’kunena kuti, ‘Tachimwa,+ tachita zolakwa,+ ndiponso tachita zinthu zoipa,’+
50 “Inu amene mwathawa lupanga, pitirizani kuthawa. Musaime chilili.+ Kumbukirani Yehova+ pamene muli kutali kwambiri ndipo mukumbukirenso Yerusalemu mumtima mwanu.”+