Deuteronomo 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+ 2 Mbiri 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye atasautsika mumtima mwake chifukwa cha zimenezi,+ anakhazikitsa pansi mtima wa Yehova Mulungu wake+ ndipo anadzichepetsa+ kwambiri pamaso pa Mulungu wa makolo ake.
29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+
12 Iye atasautsika mumtima mwake chifukwa cha zimenezi,+ anakhazikitsa pansi mtima wa Yehova Mulungu wake+ ndipo anadzichepetsa+ kwambiri pamaso pa Mulungu wa makolo ake.