2 Mbiri 6:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 ndiyeno iwo akazindikira kulakwa kwawo m’dziko limene anawatengeralo n’kulapa, ndipo akapempha chifundo kwa inu m’dziko limene akukhalamo monga anthu ogwidwa,+ n’kunena kuti, ‘Tachimwa,+ tachita zolakwa,+ ndiponso tachita zinthu zoipa,’+
37 ndiyeno iwo akazindikira kulakwa kwawo m’dziko limene anawatengeralo n’kulapa, ndipo akapempha chifundo kwa inu m’dziko limene akukhalamo monga anthu ogwidwa,+ n’kunena kuti, ‘Tachimwa,+ tachita zolakwa,+ ndiponso tachita zinthu zoipa,’+