Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 31:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachititsa nyumba ya Isiraeli ndi nyumba ya Yuda kukhalanso ndi anthu ochuluka ndiponso ziweto zochuluka,” watero Yehova.+

  • Hoseya 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamenepo ndidzamufesa ngati mbewu zanga padziko lapansi.+ Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo+ ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Inu ndinu anthu anga,”+ ndipo iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+

  • Mika 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Otsala a Yakobo,+ pakati pa mitundu yambiri ya anthu, adzakhala ngati mame ochokera kwa Yehova.+ Iwo adzakhala ngati mvula yamvumbi imene ikuwaza pazomera,+ yomwe sidalira munthu kapena kuyembekezera ana a anthu ochokera kufumbi.+

  • Machitidwe 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Komabe, amene anabalalitsidwa aja anapita m’zigawozo akulengeza uthenga wabwino wa mawu opatulika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena