Salimo 72:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzatsika ngati mvula pa udzu umene wadulidwa,+Ngati mvula yambiri yamvumbi imene imanyowetsa kwambiri nthaka.+ Yesaya 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ndidzapatsa madzi munthu waludzu,+ ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi pamalo ouma.+ Ndidzatsanulira mzimu wanga pambewu yako+ ndi madalitso anga pa mbadwa zako. 1 Akorinto 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ineyo ndinabzala,+ Apolo anathirira,+ koma Mulungu ndiye anakulitsa.+
6 Adzatsika ngati mvula pa udzu umene wadulidwa,+Ngati mvula yambiri yamvumbi imene imanyowetsa kwambiri nthaka.+
3 Pakuti ndidzapatsa madzi munthu waludzu,+ ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi pamalo ouma.+ Ndidzatsanulira mzimu wanga pambewu yako+ ndi madalitso anga pa mbadwa zako.