Deuteronomo 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malangizo anga adzagwa ngati mvula,+Mawu anga adzatsika ngati mame,+Ngati mvula yowaza pa udzu,+Ngatinso mvula yamphamvu pazomera.+ Salimo 110:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+
2 Malangizo anga adzagwa ngati mvula,+Mawu anga adzatsika ngati mame,+Ngati mvula yowaza pa udzu,+Ngatinso mvula yamphamvu pazomera.+
3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+