Mika 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Otsala a Yakobo,+ pakati pa mitundu yambiri ya anthu, adzakhala ngati mame ochokera kwa Yehova.+ Iwo adzakhala ngati mvula yamvumbi imene ikuwaza pazomera,+ yomwe sidalira munthu kapena kuyembekezera ana a anthu ochokera kufumbi.+
7 “Otsala a Yakobo,+ pakati pa mitundu yambiri ya anthu, adzakhala ngati mame ochokera kwa Yehova.+ Iwo adzakhala ngati mvula yamvumbi imene ikuwaza pazomera,+ yomwe sidalira munthu kapena kuyembekezera ana a anthu ochokera kufumbi.+