Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 “Posunga tsitsi lalitali mu Isiraeli monga lumbiro la nkhondo,

      Chifukwa cha kudzipereka mwaufulu kwa anthu,+

      Tamandani Yehova.+

  • Salimo 119:108
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 108 Inu Yehova, chonde kondwerani ndi nsembe zaufulu za pakamwa panga,+

      Ndipo ndiphunzitseni zigamulo zanu.+

  • Yesaya 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kenako ndinayamba kumva mawu a Yehova akufunsa kuti: “Kodi nditumiza ndani, ndipo ndani apite m’malo mwa ife?”+ Ine ndinayankha kuti: “Ine ndilipo! Nditumizeni.”+

  • Mateyu 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Nthawi yomweyo iwo anasiya maukonde awo+ n’kumutsatira.

  • Luka 5:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pamenepo Leviyo anasiya chilichonse,+ ndipo ananyamuka n’kumutsatira.

  • 1 Akorinto 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndikachita zimenezi mwaufulu,+ ndili ndi mphoto.+ Koma ndikachita motsutsana ndi kufuna kwanga, sindingachitire mwina, ndinebe woyang’anira mogwirizana ndi udindo+ umene unaikidwa m’manja mwanga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena