Oweruza 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Baraki anasonkhanitsa pamodzi fuko la Zebuloni+ ndi fuko la Nafitali ku Kedesi, moti amuna 10,000 anam’tsatira,+ ndipo Debora nayenso anapita nawo. Salimo 110:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+
10 Ndipo Baraki anasonkhanitsa pamodzi fuko la Zebuloni+ ndi fuko la Nafitali ku Kedesi, moti amuna 10,000 anam’tsatira,+ ndipo Debora nayenso anapita nawo.
3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+