Ekisodo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho Yetero anati: “Yehova adalitsike, iye amene anakulanditsani m’manja mwa Aiguputo ndiponso m’dzanja la Farao, amenenso analanditsa anthuwa m’manja mwa Aiguputo.+ 2 Mbiri 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa tsiku lachinayi anasonkhana pachigwa cha Beraka ndipo kumeneko anatamanda Yehova.+ N’chifukwa chake malowo anawatcha dzina+ lakuti chigwa cha Beraka* mpaka lero. Salimo 145:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakutamandani tsiku lonse.+Ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
10 Choncho Yetero anati: “Yehova adalitsike, iye amene anakulanditsani m’manja mwa Aiguputo ndiponso m’dzanja la Farao, amenenso analanditsa anthuwa m’manja mwa Aiguputo.+
26 Pa tsiku lachinayi anasonkhana pachigwa cha Beraka ndipo kumeneko anatamanda Yehova.+ N’chifukwa chake malowo anawatcha dzina+ lakuti chigwa cha Beraka* mpaka lero.