Maliko 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Petulo anayamba kumuuza kuti: “Onani! Ife tinasiya zinthu zonse ndipo takhala tikukutsatirani.”+ Luka 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma Petulo ananena kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zathu ndi kukutsatirani.”+