-
1 Samueli 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Yehova anaitananso kachitatu kuti: “Samueli!” Pamenepo Samueli anadzuka ndi kupita kwa Eli, n’kunenanso kuti: “Ndabwera, chifukwa mwandiitana ndithu.”
Atatero, Eli anazindikira kuti Yehova ndi amene anali kuitana mwanayo.
-