Miyambo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+ Hoseya 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzakhala ngati mame kwa Isiraeli,+ ndipo iye adzaphuka ngati maluwa okongola. Mizu yake idzazama ngati mtengo wa ku Lebanoni.
12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+
5 Ine ndidzakhala ngati mame kwa Isiraeli,+ ndipo iye adzaphuka ngati maluwa okongola. Mizu yake idzazama ngati mtengo wa ku Lebanoni.