Hagai 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi mbewu zilipobe m’dzenje losungiramo mbewu?+ Kodi mitengo ya mpesa, mitengo ya mkuyu, mitengo ya makangaza* ndi mitengo ya maolivi ikuberekabe zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+
19 Kodi mbewu zilipobe m’dzenje losungiramo mbewu?+ Kodi mitengo ya mpesa, mitengo ya mkuyu, mitengo ya makangaza* ndi mitengo ya maolivi ikuberekabe zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+