Deuteronomo 28:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 “Chotero, monga mmene Yehova anasangalalira kuti akuchitireni zabwino ndi kukuchulukitsani,+ momwemonso adzasangalala kuti akuwonongeni ndi kukufafanizani.+ Pamenepo mudzatheratu m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.+ Yeremiya 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndidzakondwera nawo ndi kuwachitira zabwino.+ Ndidzawabzala m’dziko lino+ mokhulupirika ndi mtima wanga wonse komanso ndi moyo wanga wonse.’”
63 “Chotero, monga mmene Yehova anasangalalira kuti akuchitireni zabwino ndi kukuchulukitsani,+ momwemonso adzasangalala kuti akuwonongeni ndi kukufafanizani.+ Pamenepo mudzatheratu m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.+
41 Ndidzakondwera nawo ndi kuwachitira zabwino.+ Ndidzawabzala m’dziko lino+ mokhulupirika ndi mtima wanga wonse komanso ndi moyo wanga wonse.’”