Yeremiya 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova wanena kuti: “Anthu onse oipa amene ndinayandikana nawo + amene akukhudza cholowa chimene ndinapatsa anthu anga Aisiraeli kuti chikhale chawo,+ ndikuwazula pamalo awo.+ Ndidzazula nyumba ya Yuda pakati pawo.+ Yeremiya 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+
14 Yehova wanena kuti: “Anthu onse oipa amene ndinayandikana nawo + amene akukhudza cholowa chimene ndinapatsa anthu anga Aisiraeli kuti chikhale chawo,+ ndikuwazula pamalo awo.+ Ndidzazula nyumba ya Yuda pakati pawo.+
7 Pa nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+