Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 79:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Anthu oyandikana nafe akutitonza,+

      Anthu otizungulira akutinyoza ndi kutiseka.+

  • Yeremiya 48:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 ‘Muledzeretseni+ anthu inu chifukwa wadzikuza pamaso pa Yehova.+ Mowabu wadzigwetsa ndipo wagubuduka m’masanzi ake,+ ndipo wakhaladi chinthu chotonzedwa.

  • Ezekieli 25:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Uuze ana a Amoniwo kuti, ‘Imvani mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Chifukwa chakuti malo anga opatulika adetsedwa, inu mwanena kuti: Eyaa! Zakhala bwino! Mwaneneranso zimenezi dziko la Isiraeli chifukwa chakuti lakhala bwinja, komanso nyumba ya Yuda chifukwa chakuti anthu ake atengedwa ukapolo.+

  • Zefaniya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Ndamva chitonzo cha Mowabu+ ndi mawu onyoza a ana a Amoni+ amene anali kunena kwa anthu anga. Iwo anali kuopseza anthu anga modzitukumula kuti awalanda dziko lawo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena