Salimo 44:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwatisandutsa chitonzo kwa anthu oyandikana nafe,+Mwatisandutsa chinthu chonyozeka ndi choseketsa kwa onse otizungulira.+ Salimo 80:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwachititsa kuti anthu oyandikana nafe azimenyana polimbirana ifeyo.+Ndipo adani athu akupitirizabe kutinyoza mmene akufunira.+
13 Mwatisandutsa chitonzo kwa anthu oyandikana nafe,+Mwatisandutsa chinthu chonyozeka ndi choseketsa kwa onse otizungulira.+
6 Mwachititsa kuti anthu oyandikana nafe azimenyana polimbirana ifeyo.+Ndipo adani athu akupitirizabe kutinyoza mmene akufunira.+