Oweruza 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno chifukwa chakuti mitima yawo inali yosangalala,+ anayamba kunena kuti: “Itanani Samisoni kuti adzatisangalatse.”+ Chotero anaitana Samisoni ndipo anam’tulutsa m’ndende kuti awachitire masewera.+ Atabwera anamuimiritsa pakati pa zipilala. Salimo 79:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu oyandikana nafe akutitonza,+Anthu otizungulira akutinyoza ndi kutiseka.+
25 Ndiyeno chifukwa chakuti mitima yawo inali yosangalala,+ anayamba kunena kuti: “Itanani Samisoni kuti adzatisangalatse.”+ Chotero anaitana Samisoni ndipo anam’tulutsa m’ndende kuti awachitire masewera.+ Atabwera anamuimiritsa pakati pa zipilala.