Yobu 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano ine ndakhala mutu wa nyimbo yawo,+Ndipo kwa iwo ndine chinthu choseketsa.+ Salimo 35:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atandiona ndikuyenda motsimphina anasangalala ndipo anasonkhana pamodzi.+Anasonkhana pamodzi kuti alimbane nane.+Anandimenya pamene sindinali kuyembekezera.+Anandikhadzulakhadzula ndipo sanakhale chete.+ Salimo 69:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu okhala kuchipata anayamba kundidera nkhawa,+Ndipo anthu amene anali kumwa zakumwa zoledzeretsa anali kundinena mu nyimbo zawo.+ Aheberi 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+
15 Atandiona ndikuyenda motsimphina anasangalala ndipo anasonkhana pamodzi.+Anasonkhana pamodzi kuti alimbane nane.+Anandimenya pamene sindinali kuyembekezera.+Anandikhadzulakhadzula ndipo sanakhale chete.+
12 Anthu okhala kuchipata anayamba kundidera nkhawa,+Ndipo anthu amene anali kumwa zakumwa zoledzeretsa anali kundinena mu nyimbo zawo.+
36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+