Yobu 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano ine ndakhala mutu wa nyimbo yawo,+Ndipo kwa iwo ndine chinthu choseketsa.+ Maliko 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso anali kum’menya m’mutu ndi bango ndi kumulavulira, ndipo anali kugwada ndi kumuweramira.+