Yobu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye wandisandutsa mwambi+ wa anthu,Mwakuti ndakhala munthu womulavulira kumaso.+