Yobu 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano ine ndakhala mutu wa nyimbo yawo,+Ndipo kwa iwo ndine chinthu choseketsa.+ Salimo 69:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene ndinavala ziguduli,Ndinakhala ngati mwambi kwa iwo.+