Salimo 69:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu okhala kuchipata anayamba kundidera nkhawa,+Ndipo anthu amene anali kumwa zakumwa zoledzeretsa anali kundinena mu nyimbo zawo.+ Maliro 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndakhala chinthu choseketsa+ kwa anthu onse odana nane, ndipo amandiimba m’nyimbo yawo tsiku lonse.+
12 Anthu okhala kuchipata anayamba kundidera nkhawa,+Ndipo anthu amene anali kumwa zakumwa zoledzeretsa anali kundinena mu nyimbo zawo.+
14 Ndakhala chinthu choseketsa+ kwa anthu onse odana nane, ndipo amandiimba m’nyimbo yawo tsiku lonse.+