Yobu 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano ine ndakhala mutu wa nyimbo yawo,+Ndipo kwa iwo ndine chinthu choseketsa.+ Salimo 69:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu okhala kuchipata anayamba kundidera nkhawa,+Ndipo anthu amene anali kumwa zakumwa zoledzeretsa anali kundinena mu nyimbo zawo.+ Salimo 137:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kumeneko, amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Ndipo otinyozawo anatipempha kuti tiwasangalatse.+ Iwo anati:“Tiimbireni imodzi mwa nyimbo za ku Ziyoni.”+
12 Anthu okhala kuchipata anayamba kundidera nkhawa,+Ndipo anthu amene anali kumwa zakumwa zoledzeretsa anali kundinena mu nyimbo zawo.+
3 Kumeneko, amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Ndipo otinyozawo anatipempha kuti tiwasangalatse.+ Iwo anati:“Tiimbireni imodzi mwa nyimbo za ku Ziyoni.”+