Yobu 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Tsopano anthu amene ndi ana aang’ono poyerekeza ndi ine,+Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu oweta nkhosa zanga. Salimo 44:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwatisandutsa chitonzo kwa anthu oyandikana nafe,+Mwatisandutsa chinthu chonyozeka ndi choseketsa kwa onse otizungulira.+ Yeremiya 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwandidabwitsa inu Yehova, ndipo ndadabwa. Mwagwiritsa ntchito mphamvu zanu pa ine ndipo mwapambana.+ Ndakhala chinthu choseketsa tsiku lonse. Aliyense akungondinyoza.+
30 “Tsopano anthu amene ndi ana aang’ono poyerekeza ndi ine,+Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu oweta nkhosa zanga.
13 Mwatisandutsa chitonzo kwa anthu oyandikana nafe,+Mwatisandutsa chinthu chonyozeka ndi choseketsa kwa onse otizungulira.+
7 Mwandidabwitsa inu Yehova, ndipo ndadabwa. Mwagwiritsa ntchito mphamvu zanu pa ine ndipo mwapambana.+ Ndakhala chinthu choseketsa tsiku lonse. Aliyense akungondinyoza.+