Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ine ndakhala chinthu choseketsa kwa anthu anzanga,+

      Ndakhala munthu woitana kwa Mulungu kuti amuyankhe.+

      Munthu wolungama ndi wosalakwa wakhala choseketsa.

  • Salimo 22:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+

      Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati:

  • Yeremiya 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsoka ine,+ chifukwa inu mayi anga munabereka ine munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndipo ndimalimbana ndi dziko lonse.+ Sindinapereke ngongole komanso sanandikongoze kalikonse, koma anthu onse akunditemberera.+

  • Maliro 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndakhala chinthu choseketsa+ kwa anthu onse odana nane, ndipo amandiimba m’nyimbo yawo tsiku lonse.+

  • Machitidwe 17:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ndiyeno anthuwo atamva za kuuka kwa akufa, ena anayamba kuseka monyodola,+ pamene ena anati: “Chabwino, udzatiuzenso zimenezi nthawi ina.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena