Yobu 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+ Yobu 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndithu, onyoza andizungulira,+Ndipo diso langa likuyang’anitsitsa khalidwe lawo lopanduka. Yobu 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Tsopano anthu amene ndi ana aang’ono poyerekeza ndi ine,+Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu oweta nkhosa zanga. Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati: Aheberi 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+
10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+
30 “Tsopano anthu amene ndi ana aang’ono poyerekeza ndi ine,+Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu oweta nkhosa zanga.
7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati:
36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+