Yobu 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pa zimenezi m’pamene Yobu anatsegula pakamwa pake n’kuyamba kutemberera tsiku limene anabadwa.+ Yeremiya 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Litembereredwe tsiku limene ndinabadwa! Tsiku limene mayi anga anandibereka lisadalitsike!+
3 Pambuyo pa zimenezi m’pamene Yobu anatsegula pakamwa pake n’kuyamba kutemberera tsiku limene anabadwa.+