Yobu 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Liwonongeke tsiku limene ndinabadwa,+Ndiponso usiku umene wina ananena kuti, ‘Mwamuna wamphamvu wapangika m’mimba.’ Yeremiya 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsoka ine,+ chifukwa inu mayi anga munabereka ine munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndipo ndimalimbana ndi dziko lonse.+ Sindinapereke ngongole komanso sanandikongoze kalikonse, koma anthu onse akunditemberera.+
3 “Liwonongeke tsiku limene ndinabadwa,+Ndiponso usiku umene wina ananena kuti, ‘Mwamuna wamphamvu wapangika m’mimba.’
10 Tsoka ine,+ chifukwa inu mayi anga munabereka ine munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndipo ndimalimbana ndi dziko lonse.+ Sindinapereke ngongole komanso sanandikongoze kalikonse, koma anthu onse akunditemberera.+