Yobu 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Zikanakhala bwino tsiku limene ndinabadwa likanapanda kufika,+Ndiponso usiku umene wina ananena kuti: ‘Mwamuna wapangika mʼmimba.’
3 “Zikanakhala bwino tsiku limene ndinabadwa likanapanda kufika,+Ndiponso usiku umene wina ananena kuti: ‘Mwamuna wapangika mʼmimba.’