Yobu 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Liwonongeke tsiku limene ndinabadwa,+Ndiponso usiku umene wina ananena kuti, ‘Mwamuna wamphamvu wapangika m’mimba.’
3 “Liwonongeke tsiku limene ndinabadwa,+Ndiponso usiku umene wina ananena kuti, ‘Mwamuna wamphamvu wapangika m’mimba.’