Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kodi munanditulutsiranji m’mimba?+

      Zikanakhala bwino ndikanafa kuti diso ndi limodzi lomwe lisandione.

  • Yeremiya 15:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsoka ine,+ chifukwa inu mayi anga munabereka ine munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndipo ndimalimbana ndi dziko lonse.+ Sindinapereke ngongole komanso sanandikongoze kalikonse, koma anthu onse akunditemberera.+

  • Yeremiya 20:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Atembereredwe munthu amene anabweretsa uthenga wabwino kwa bambo anga powauza kuti: “Mkazi wako wakuberekera mwana wamwamuna.” Munthuyo anawasangalatsa kwambiri bambo anga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena