Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+ Luka 1:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Anthu oyandikana naye ndi abale ake anamva kuti Yehova anam’chitira chifundo chachikulu,+ ndipo anayamba kukondwera+ naye pamodzi.
58 Anthu oyandikana naye ndi abale ake anamva kuti Yehova anam’chitira chifundo chachikulu,+ ndipo anayamba kukondwera+ naye pamodzi.