Genesis 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako, Esau anakweza maso ake n’kuona akazi ndi ana. Ndiyeno anafunsa Yakobo kuti: “Nanga amene uli nawowa ndani?” Iye anayankha kuti: “Amenewa ndi ana amene Mulungu wapatsa ine kapolo wanu.”+ Genesis 48:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo anandiuza kuti, ‘Ndidzakupatsa ana,+ ndipo mwa iwe mudzatuluka mitundu yambiri ya anthu.+ Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako kuti lidzakhale dziko lawo mpaka kalekale.’+ 1 Samueli 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndipo Yehova anakomera mtima Hana,+ moti anayamba kutenga pakati ndipo anabereka ana aamuna atatu ndi aakazi awiri.+ Mwanayo Samueli anapitiriza kukula, akukondedwa ndi Yehova.+ 1 Mbiri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo pa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu+ wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.
5 Kenako, Esau anakweza maso ake n’kuona akazi ndi ana. Ndiyeno anafunsa Yakobo kuti: “Nanga amene uli nawowa ndani?” Iye anayankha kuti: “Amenewa ndi ana amene Mulungu wapatsa ine kapolo wanu.”+
4 Ndipo anandiuza kuti, ‘Ndidzakupatsa ana,+ ndipo mwa iwe mudzatuluka mitundu yambiri ya anthu.+ Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako kuti lidzakhale dziko lawo mpaka kalekale.’+
21 ndipo Yehova anakomera mtima Hana,+ moti anayamba kutenga pakati ndipo anabereka ana aamuna atatu ndi aakazi awiri.+ Mwanayo Samueli anapitiriza kukula, akukondedwa ndi Yehova.+
5 Ndipo pa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu+ wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.