Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 13:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Patapita nthawi, mkaziyo anabereka mwana wamwamuna ndipo dzina lake anamutcha kuti Samisoni.+ Mnyamatayo anali kukula, ndipo Yehova anapitiriza kumudalitsa.+

  • 1 Samueli 2:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Izi zili choncho, mwanayo Samueli anali kukula ndi kukondedwa kwambiri ndi Yehova komanso anthu.+

  • 1 Samueli 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Samueli anapitiriza kukula ndipo Yehova anali naye,+ moti palibe mawu ake alionse amene anapita padera.+

  • Luka 1:80
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 80 Choncho mwana uja anakulirakulira+ ndipo anali kulimba mwauzimu. Iye anali kukhala m’zipululu mpaka tsiku lakuti adzionetsere poyera kwa Isiraeli.

  • Luka 2:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Koma Yesu anali kukulabe m’nzeru+ ndi mu msinkhu. Ndipo Mulungu ndi anthu anapitiriza kukondwera naye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena