Miyambo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ukamvetsera nzeru ndi khutu lako,+ ukaika mtima wako pa kuzindikira,+ Miyambo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 udzamvetsa tanthauzo la kuopa+ Yehova ndipo udzamudziwadi Mulungu.+ Yesaya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+ mzimu wanzeru,+ womvetsa zinthu,+ wolangiza, wamphamvu,+ wodziwa zinthu+ ndi woopa Yehova.+
2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+ mzimu wanzeru,+ womvetsa zinthu,+ wolangiza, wamphamvu,+ wodziwa zinthu+ ndi woopa Yehova.+