Luka 2:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Koma Yesu anali kukulabe m’nzeru+ ndi mu msinkhu. Ndipo Mulungu ndi anthu anapitiriza kukondwera naye.+ 1 Akorinto 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma inu muli ogwirizana ndi Khristu Yesu chifukwa cha Mulunguyo. Yesuyo amatisonyeza nzeru+ za Mulungu ndiponso chilungamo+ cha Mulungu. Kudzera mwa Yesu, anthu akhoza kuyeretsedwa,+ ndipo kudzera mwa dipo* akhoza kumasulidwa,+
52 Koma Yesu anali kukulabe m’nzeru+ ndi mu msinkhu. Ndipo Mulungu ndi anthu anapitiriza kukondwera naye.+
30 Koma inu muli ogwirizana ndi Khristu Yesu chifukwa cha Mulunguyo. Yesuyo amatisonyeza nzeru+ za Mulungu ndiponso chilungamo+ cha Mulungu. Kudzera mwa Yesu, anthu akhoza kuyeretsedwa,+ ndipo kudzera mwa dipo* akhoza kumasulidwa,+