Yohane 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+ Yohane 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mthandiziyo akadzafika, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani m’choonadi chonse. Pakuti sadzalankhula zongoganiza mwa iye yekha, koma adzalankhula zimene wazimva, ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+
17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+
13 Koma mthandiziyo akadzafika, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani m’choonadi chonse. Pakuti sadzalankhula zongoganiza mwa iye yekha, koma adzalankhula zimene wazimva, ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+