Yohane 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mthandiziyo akadzabwera, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani mʼchoonadi chonse. Chifukwa sadzalankhula zongoganiza payekha, koma adzalankhula zimene wamva ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:13 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 49-50 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 324/1/2000, ptsa. 8-99/1/1990, tsa. 8
13 Koma mthandiziyo akadzabwera, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani mʼchoonadi chonse. Chifukwa sadzalankhula zongoganiza payekha, koma adzalankhula zimene wamva ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+
16:13 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 49-50 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 324/1/2000, ptsa. 8-99/1/1990, tsa. 8