Yohane 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kunena zoona, ndikupita kuti inu mupindule. Chifukwa ngati sindipita ndiye kuti mthandizi uja+ sabwera kwa inu. Koma ndikapita ndikamutumiza kwa inu.
7 Kunena zoona, ndikupita kuti inu mupindule. Chifukwa ngati sindipita ndiye kuti mthandizi uja+ sabwera kwa inu. Koma ndikapita ndikamutumiza kwa inu.