Miyambo 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aliyense wosalankhulapo mawu ake ndi wodziwa zinthu,+ ndipo munthu wozindikira amakhala wofatsa.+ Aefeso 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa chifukwa chimenechi, lekani kukhala opanda nzeru, koma pitirizani kuzindikira+ chifuniro+ cha Yehova. Aheberi 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu okhwima mwauzimu, amene pogwiritsa ntchito mphamvu zawo za kuzindikira,+ aphunzitsa mphamvuzo kusiyanitsa choyenera ndi chosayenera.+
17 Pa chifukwa chimenechi, lekani kukhala opanda nzeru, koma pitirizani kuzindikira+ chifuniro+ cha Yehova.
14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu okhwima mwauzimu, amene pogwiritsa ntchito mphamvu zawo za kuzindikira,+ aphunzitsa mphamvuzo kusiyanitsa choyenera ndi chosayenera.+