Aroma 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro. 1 Atesalonika 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu akufuna kuti mukhale oyera+ mwa kupewa dama.*+ 1 Atesalonika 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muziyamika+ pa chilichonse, pakuti chimenechi ndi chifuniro cha Mulungu kwa inu mwa Khristu Yesu. 1 Petulo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti pamene akukhala ndi moyo m’thupi ku nthawi yotsala ya moyo wake,+ asatsatenso zilakolako za anthu, koma chifuniro cha Mulungu.+
2 Musamatengere+ nzeru za nthawi* ino, koma sandulikani mwa kusintha maganizo anu,+ kuti muzindikire+ chimene chili chifuniro+ cha Mulungu, chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.
2 kuti pamene akukhala ndi moyo m’thupi ku nthawi yotsala ya moyo wake,+ asatsatenso zilakolako za anthu, koma chifuniro cha Mulungu.+