Aroma 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mulungu adzatero kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu.+ Chotero, m’maganizo mwanga ineyo ndine kapolo wa chilamulo cha Mulungu,+ koma m’thupi langa ndine kapolo wa chilamulo cha uchimo.+ Aefeso 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo munaphunzitsidwa kuti mukhale atsopano mu mphamvu yoyendetsa maganizo anu,+
25 Mulungu adzatero kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu.+ Chotero, m’maganizo mwanga ineyo ndine kapolo wa chilamulo cha Mulungu,+ koma m’thupi langa ndine kapolo wa chilamulo cha uchimo.+